On Nyasa VoiceBox, Bon Kalindo discusses the challenges facing Malawians and urges opposition leaders to form a coalition that includes the former Second Lady, Madam Mary Chilima. He insists that she is the crucial element needed to unlock a successful campaign against the MCP in 2025.
Ku Nyasa Voicebox, a Bon Kalindo akambiran za mavuto omwe aMalawi akukumana nawo ndipo apempha atsogoleri otsutsa kuti apange mgwirizano womwe ukuphatikizapo Madam Mary Chilima. Iye akuumirira kuti Mayi Chilima ndi key kuti atsegule kampeni yabwino yolimbana ndi MCP mu 2025.
#malawi
Ещё видео!