(Intro)
“Ngati Sumafila Zomwe ndimapanga ingotseka Maso “ x 2
Ma Lawyer Ama Judger Nyimbo zathu
Ma Nurse sangachize flow yathu
Ma Blessings amazela njira Yathu
Ma Rasta Amafeela Chamba Chathu
Ndizovaya (yeah) x8
(Verse 1 )
Ngati Sumafila zomwe ndipanga jngoseka Maso
Line Yaku Show Ngati Fans Ikusaka Gaso
Ku chi Corner Ngati mwina Ndimaimba Dancehall
Nyimbo zavaya Kale kunja koma opanda passport
Akuuzani kuti anawo ndi smoko ndi blanda
Boys ili boys quarter kumvela boys siizamva
Akatispotta kuluza control they go wild ah iwe
Amatiwelengela taapolesa ku library yeah
Ndikufuna One On One Meeting ndi Major (one)
Ndiboys tikuyenda mma College Zau Lecture
Ati ndikusowa koma Pa Google akumandipeza
Ma Punchiline onsewa ndizosatheka Kundimenya
Squad ikuvaya hide your wifey
Kutentha, level imangosintha ngati crisis
God showed me a sign life got meaning,
G been independent
Ataiva sanaive anaiika full stop
Pano ndimifuuliro palibe funso
Ma Lawyer Ama Judger Nyimbo zathu
Ma Nurse sangachite flow yathu
Ma Blessings amazela njira Yathu
Ma Rasta Amafeela Chamba Chathu
Ndizovaya (yeah) x8
(Verse 2 )
Hustle ndi chifukwa chokwanila kukhalira moyo
Nde ndikuuzeni facts ndilibe nanu zifukwa madolo
Ndikufuna rack, girls ikuonesa titties
Manja anga akuyabwa maso akuyang'ana business
Ukamva Spee ndi dirt
Ma style ndi Plenty
Ndima Boss akowo mwa ife utha kulowa mo ka 20
Milion
Sungatipeze or utamanya liwiro
Uzingotinta ndi kuimba Rhumba ngati awilo
Tili lit ngati Chibiliti osati Litiro ( liti? )
Huh? I’m a leader 123 u follow (4)
Game Tima Runner Ngati Tikuthawa Po po
Ife Tinavaya iwe Tangoona uli Pompo Pompo
Ati spe uli spe Dirty flo u got The Flow Thats my Bro bro
Too turned up on a weekend
Imposter mutsitseni
Oh ma days famous potokola bass
Akufuna piece/peace ife tikugawa mizongo
Zikusinja mitondo we fully in fully reloaded pho! pho! pho! pho! pho!
Ma Lawyer Ama Judger Nyimbo zathu
Ma Nurse sangachite flow yathu
Ma Blessings amazela njira Yathu
Ma Rasta Amafeela Chamba Chathu
Ndizovaya (yeah) x8
Produced by Famous
Directed by Major , Star films
Team
David Major
K1 $mollet
Nguko
OG
Dirty flo
Georjiz
Famous
Crispy Malawi
Ife Ndi Amalawi Ent. / Surf music® 2023
Ещё видео!